7 people supporting this
Clever James chabukukais raising support directly
Community campaign
NDITHANDIZENI KUTI NDIPITIRIZE MAPHUNZIRO ANGA KU MZUZU UNIVERSITY
About this campaign
Dzina langa ndine Clever James Chabukuka. Ndinalemba mayeso anga a MSCE mu 2025 ndipo, mwa chisomo cha Mulungu, ndinakhoza 16 points. Mwachosomo cha Mulungu , ntapanga apply za NCHE, sankhidwira ku Mzuzu University, komwe ndikupanga Bachelor of Science in Education (reg # BEDSDL2126)
Za Loans Board zitatluka, napanga nawo apply koma mwatsoka ndinasidwa zonse Tuition Fees ndi Upkeed. Ngakhale zinali choncho, sindinataye mtima. Ndinayesetsa kupempha thandizo kwa anthu osiyanasiyana, kuphatikizapo timothy social welfare ku Mzuni, kuti andithandize kundipangira post nkhani yanga pa page yake kuti anthu akufuna kwa bwino andithandize
Mwa thandizo la anthu abwino, ndinakwanitsa kupeza ndalama zoyendera kuchokera ku Karonga kubwera ku Mzuzu komanso zolipirira nyumba (accommodation). Ndinapezanso munthu amene anandilonjeza kuti azindilipirira fees mpaka nditamaliza school
Pano munthu anandilonjeza wandiuza kuti akukumananso ndi mavuto azachuma ndipo sangathe kupitiriza kundithandiza. Izi zandiika pa vuto lalikulu chifukwa ndili pachiwopsezo chosiya sukulu chifukwa chosowa ndalama
Ndakulira m’mavuto ndipo ndilibe makolo. Panopa ndimakhala ndi agogo anga aakazi, omwe nawonso nawonso sangwanise kundithandize kulipira fees yanga.ndimakhulupilira kuti school ndi njira imoz yodalilika yomwe ingathe kusintha nyengo zanga
Chonde ndithandizeni kuti maloto anga asathe chifukwa chosowa fees. Ndikupempha aliyense amene angathe kundithandiza, kaya ndi ndalama kapena njira ina iliyonse, kuti ndikwanise kupitiriza school yanga
Ndalama zomwe ndikufunikira pa semester ndi MKMK600,000, ndipo pa academic year ndi pafupifupi MK1,200,000
Thandizo lililonse, ngakhale litakhala laling’ono, lingandithandize kwambiri. Ndikuthokoza kuchokera pansi pa mtima kwa aliyense amene angandithandize kapena kugawana uthengawu ndi anthu ena.
Pa thandizo kapena mafunso, chonde nditumizireni pa nambala iyi:
+265 999 40 06 50.
account yanga yaku school ndi imeneyi
Mulungu akudalitseni nonse chifukwa cha mtima wanu wothandiza

- Name of the Bank: FDH Bank
- Account Name : MZUNI New CODeL Fees Collection
- Account
- Account Number : 1470000597856
- Branch : Mzuzu Service Centre
- Registration Number yanga : BEDSDL2126)
Mulungu akudalitseni nonse chifukwa cha mtima wanu wothandiza
Photos
Watch the story
MK 5,250
raised of MK 1,368,422 goal
0.4%
funded
7 people supporting this campaign
Supporting nowSupport this campaign
Popular
MK
Your details - name and email are optional
Reciva
You supports
MK 2,000
to
Clever James chabukuka
+ MK 62 processing fee · you'll be charged MK 2,062
Pay instantly with mobile money or a card.
Payments secured by![]()
SecuredCommunity backed100% to Clever
Recent support
7 supporters
Nice
MK 1,000
20 Oct 2026
I need this guy to learn
Anonymous
MK 500
20 Oct 2026
Anonymous
MK 2,000
20 Oct 2026
Anonymous
MK 50
20 Oct 2026
Ausman
MK 200
20 Oct 2026
Have something you're raising money for?
Create your own Reciva campaign and start receiving support from your community.
Create your campaignPowered by
· free to start