4 people supporting this
Mike Paul Khomaniis raising support directly
Community campaign
Raising fund for accommodation and school materials
About this campaign
Those who wish well help me. Dzina langa ndine, Mike Paul Khomani, kuchokera by mmudzi mwa mazira, mdera la mfumu yaikulu Ganya. Mboma la Ntcheu. Bambo anga anamwalira mu chaka cha 2019 pomwe mayi anga anamwalira chaka 2023.
Pano ndimakhala ndi Agogo anga amuna omwe ndi a zaka 74 komanso akazi omwe ndi a zaka 71.
Ndinakwanitsa kuphunzira ku Ntcheu secondary school komwe ndinasankhidwira Kaamba koti ndinapeza mwayi ophunzira pa bursary ya mphungu WA kunyumba yamalamulo mpaka form 4.
Nditamva zokhudza nche kuchokera kwa mnzanga sindinazengereze.
Ndi nkhani yosangalatsa kuti ndinasankhidwira ku university of Malawi... Kuti ndikapange study bachelor of education language. (odel)
Ngakhaletu zinthu I zili zokondweretsa chotere,, ndili ndi vuto la ndalama yolipirira malo okhala komanso zinthu Zina zofunika ku school..
Ndinalembera kupempha ngongole ku bungwe lotchedwa Higher Education Student Grants Board... Anakwanitsa kundiloleza tuition yokha..m
Agogo anga sangakwanitse kundipatsa ndalama ya rent komanso zipangizo Zina za school. Your contribution will have a great impact on my education journey.

Photos
MK 3,400
raised of MK 600,000 goal
0.6%
funded
4 people supporting this campaign
Giving nowGive your support
MK
Your details - name and email are optional
Reciva
You gives
MK 2,000
to
Mike Paul Khomani
+ MK 62 processing fee · you'll be charged MK 2,062
Pay instantly with mobile money or a card.
Payments secured by![]()
SecuredCommunity backed100% to Mike
Recent support
Latest supporters and messages.
Anonymous
31 Aug 2026
MK 300
No message provided.
Anonymous
31 Aug 2026
MK 100
No message provided.
Anonymous
31 Aug 2026
MK 2,000
No message provided.
Anonymous
31 Aug 2026
MK 1,000
No message provided.
Have something you're raising money for?
Create your own Reciva campaign and start receiving support from your community.
Create your campaignPowered by
· free to start