MedicalHelp Catherine Kawerere with her medical bills
Catherine Kawerere ndi mtsikana wa ku Kasungu ali pululu waukulu omwe wavutika nao kwazaka 7. Iyeyo kidney yake yidafoka ndipo wakhala akupita kuchipatala koma tsopano zafika poti akufunika akapeza thandizo Ku India komwe kidney transplant ikatheke. Abale ndi alongo zotheka kupulumusa moyo wamzathu munyengo yovutayi chifukwa iyeyo akusowekera 46 million kuti zonse zitheke. Dziwani kuti or 1 thousand ikhoza kusutha ndithu mpaka kupeza ndalama yonse.Ndikangachape mulinako kangathe kuthandiza kupulumutsa moyo wa cathy








