Reciva logo
How it worksBrowse campaignsPricingFAQ
Log inStart a campaign
Reciva logo
TermsPrivacyContactLive chat
Secured byPayChanguPayChangu

© 2026 Reciva. All rights reserved.Made with

All campaigns

Support a cause, or start your own. Start a campaign

MK 190,085

Raised across the platform

8

Active campaigns

163

Supporters

All categoriesEducationMedicalCommunityEmergencyBusinessOther
Sort byMost recentMost fundedEnding soon

Showing 1–1 of 1 campaigns

Education at Matewere VillageEducation

Education at Matewere Village

Dzina langa ndine Benson Tambuli from Mangochi  ndinalemba mayeso anga a form 4 mu chaka cha 2024 ndipo ndinakhoza 24 points kuchokera pa school inayake ndipo ine ndimaphunzirapo pa school po chifukwa choti anandipasa busury chifukwa cha kulimbikira ndipo ku school zimatheka ndithu kwambiri . After mayeso atatuluka amene akandiripilira school fees aja anandiuza kuti ndipange apply za NCHE komaso Domasi and Nalikule Collage of Education ndipo zinapezeka kuti andisya konse . Ine sinasiyire popo kuyesa mwayi sinatengere kuti kwanthu ndikusowekera ndinayesa mwayi kwa anthu omwe ali ndi kuthekera kuti mwina atha kundipasa mwayi opitiriza maphunziro anga chifukwa schools ndikayifuna kwambiri. Nditayenda mwa anthu omwe angakhale ndikuthekera ena amatha kundiuza kuti sangandithandize ena akandiuza kuti amathandiza anthu aku primarily okha pa busury yawo ndipo ine natengaso mwayi uwu kumupasa mwana mwa kumdera lanthu yemwe anakhoz selection ndipo pano zinatheka .  Nditayendaso kwa munthu wina anandiuza kunena kuti school itheka ndipange apply to any private university azindilipilira scholarships fees ndipo napanga maganyu ndikupanga apply ku Malawi Advertise University ( MAU) komaso ku Malawi Assemblies of God University ( MAGU) Lilongwe campus ananditenga konse umumu munali mu August 2025 . Ndipo anandiuza kuti ndipote ku MAGU ndikapange Bachelor of Business administration ndipo madongosolo onse tinapanga bwinobwino nditapita iwowo akangoti school fees atumiza kwayimbir kumangonena chimoxmox pakana matsiku a registration anadusa kenako ndinayakhulana ndi a regstar za mvuto langa li ndipo anandiuza kuti ndipange reserve place ndipo ndinapanga chimoxmox. Ine ndikumabwelera kumudzi  Ndiri kumudxi ndinawona advert from Mzuzu University ndipo ndinawona tuition fees inali pa 600,000 per year ( 300 per semester) ndipo ndinaganizir date la school kuti ndipatali ndipo ndinapanga program yanga yomwe ndikapanga ya part time classes ( from form 4 to form 1 , Std 5 to Std 8 ) ndipo ndikupanga program yangayi kuti pomazafika mu September 2026 ndizakhale tapeza tuition fee koma mwa mwayi napeza mwayi pa ka primary school inayake kuti ndikakhale phunzitsi chifukwa iwoo anali atava kale za ine kuchokera kwa anthu ena ozungulira ndipo ndinapita kuti kwinako ndizikathamangisa ma part time classes popo ndipo qnandilora kutero  Ndinayamba ntchito patatha mwenzi after kupanga apply za Muzuni ndinava za kukwera kwa tuition fee ndipo ndinawona ngati tsogolo langa lather popo .  Ndipo pano ndimafuna kwa anthu omwe ali ndi kuthekera andithandize za tuition fees chifukwa kandalam komwe ndikalandira Kathera kukhozekera zinthu zotenga school komaso ndalama ya rent .  Ku mzuzu ndikukapanga Bachelor of Business (tourism management) Nditabwera ku Lilongwe anthu ena amudzi wa kwanthu komaso Achibale Amandinena kuti bola ndiizipita ku joni za school ndizisiye zilibe phindu moti apapa akazangova zoti ndiri ku school kwa iwow sizimasangalasa moti apapa ndizachita kunena kuti ndikupita ku nyanja kukasaka ndalama My contact details: 0990374168

MK 3000.1% funded
1 supporter13 days left